Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu
Pa ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu pazikhala nkhani zophunzira, zinthu zotithandiza pa pulogalamu ya kuwerenga Baibulo kwa mlungu uliwonse ndiponso nkhani za mumsonkhano wina womwe uzichitika mlungu uliwonse.