Azimayi
Kodi azimayi ali ndi maudindo otani?
Miy 31:17, 21, 26, 27; Tit 2:4
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Ge 21:8-12—Sara ataona Isimaeli akuzunza mwana wake Isaki, anachonderera Abulahamu kuti ateteze mwana wakeyo
1Mf 1:11-21—Bati-seba atadziwa kuti ufumu komanso moyo wa mwana wake Solomo unali pangozi, anapempha Mfumu Davide kuti amuteteze
N’chifukwa chiyani tiyenera kumvera komanso kulemekeza amayi athu?
Eks 20:12; De 5:16; 27:16; Miy 1:8; 6:20-22; 23:22
Onaninso 1Ti 5:9, 10
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
1Pe 3:5, 6—Mtumwi Petulo anafotokoza kuti Sara anali ngati mayi kwa ana aakazi ambiri chifukwa anali ndi chikhulupiriro cholimba
Miy 31:1, 15, 21, 28—Mayi a Mfumu Lemueli anapereka malangizo othandiza kwa mwana wawoyu okhudza ukwati komanso udindo wa mkazi wokwatiwa ndi azimayi
2Ti 1:5; 3:15—Mtumwi Paulo anayamikira mayi ake a Timoteyo, a Yunike, chifukwa chophunzitsa mwana wawo Malemba kuchokera pamene anali wakhanda ngakhale kuti amuna awo anali osakhulupirira