Kupanda Ulemu
Kodi tiyenera kupewa kuchita zinthu ziti zosonyeza kupanda ulemu?
Onaninso Sl 74:10, 18; Yuda 8, 10
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
1Sa 2:12-17, 22-25, 27-30—Ana aamuna a Mkulu wa Ansembe Eli sankalemekeza dongosolo la Yehova lokhudza kulambira ndipo Eli analephera kuwalangiza. Zimenezi zinasonyeza kuti Eli nayenso sanalemekeze Yehova
2Mf 1:9-15—Yehova anapha asilikali omwe sanalemekeze mneneri wake Eliya koma sanaphe amene anali odzichepetsa