Makhalidwe Oipa
Kodi Akhristu ayenera kupewa kuchita zinthu zoipa ziti?
Mawu achipongwe
Mt 5:22; 1Ak 6:9, 10; Aef 4:31
Onaninso Eks 22:28; Mla 10:20; Yuda 8
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Kulandira kapena kupereka ziphuphu
Eks 23:8; Sl 26:9, 10; Miy 17:23
Onaninso De 10:17; 16:19; Sl 15:1, 5
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
1Sa 8:1-5—Ana a mneneri Samueli ankalandira ziphuphu komanso kupotoza chilungamo m’malo motengera chitsanzo chabwino cha bambo awo
-
Ne 6:10-13—Adani a anthu a Yehova analipira mneneri wonyenga dzina lake Semaya kuti aopseze Bwanamkubwa Nehemiya komanso kubwezeretsa m’mbuyo ntchito ya Yehova
-
Kudzitama
Onani “Kudzitama”
Khalidwe lopanda manyazi; khalidwe lonyansa; chiwerewere; chigololo
Onani “Chiwerewere”
Mpikisano; Kupikisana
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Mko 9:33-37; 10:35-45—Yesu anadzudzula atumwi ake mobwerezabwereza chifukwa cha khalidwe lawo lokonda mpikisano kuti apatsidwe maudindo
-
3Yo 9, 10—Diotirefe ankakonda “kukhala woyamba” pakati pa abale
-
Kuyambitsa magawano; kulimbikitsa magulu ampatuko
Kuledzera; kumwa mopitirira malire
Miy 20:1; 23:20, 29-35; 1Ak 5:11; 6:9, 10
Onaninso Aef 5:18; 1Ti 3:8; Tit 2:3; 1Pe 4:3
Onaninso “Kumwa mowa”
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Ge 9:20-25—Nowa analedzera ndipo zimenezi zinachititsa kuti Hamu ndi mwana wake Kanani achite tchimo lalikulu
-
Da 5:1-6, 30—Mfumu Belisazara ataledzera, ananyoza Yehova ndipo zotsatirapo zake anaphedwa komanso ufumu wake unatha
-
Kulanda
Sl 62:10; 1Ak 5:10, 11; 6:9, 10
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Yer 22:11-17—Yehova anadzudzula Mfumu Salumu (Yehoahazi) chifukwa cha kuba mwachinyengo, kulanda zinthu za ena ndi machimo ena akuluakulu
-
Lu 19:2, 8—Zakeyu, yemwe anali mkulu wa okhometsa misonkho, analapa machimo ake oba zinthu mwachinyengo ndipo analonjeza kuti abweza chilichonse chimene analanda
-
Mac 24:26, 27—Bwanamkubwa Felike ankaganiza kuti Mtumwi Paulo amupatsa chiphuphu koma sanatero
-
Chiphamaso kapena kudzionetsera
Yob 32:21, 22; Sl 5:9; 12:2, 3; Miy 26:24-28; 29:5
Onaninso Miy 28:23; 1At 2:3-6
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Lu 18:18, 19—Yesu anakana kuchita zinthu modzionetsera
-
Mac 12:21-23—Mfumu Herode Agiripa analolera kuti anthu azimutamanda ngati mulungu; anaphedwa chifukwa chosalemekeza Mulungu
-
Dyera
Onaninso Lu 21:34, 35
Miseche; kulowerera nkhani za eni
Miy 25:23; 1At 4:11; 2At 3:11; 1Pe 4:15
Onaninso Miy 20:19; 1Ti 5:13
Kulambira mafano
Onani “Kulambira mafano”
Kunama; kunena bodza
Onani “Kunama”
Kunama; kuneneza
Onani “Kunama”
Kugwiritsa ntchito magazi molakwika
Ge 9:4; De 12:16, 23; Mac 15:28, 29
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
1Sa 14:32-34—Aisiraeli anachimwira Yehova podya nyama asanakhetse magazi ake
-
Kupha
Onaninso Mt 5:21, 22; Mko 7:21
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Ge 4:4-16—Ngakhale kuti Yehova anapereka malangizo achikondi kwa Kaini, koma iye anapha m’bale wake Abele yemwe anali wolungama
-
1Mf 21:1-26; 2Mf 9:26—Dyera linachititsa kuti Mfumu yoipa Ahabu komanso Mfumukazi Yezebeli akonze zoti Naboti ndi ana ake aamuna aphedwe
-
Kung’ung’udza
Onaninso Nu 11:1
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Nu 14:1-11, 26-30—Pamene Aisiraeli anayamba kung’ung’udzira Mose ndi Aroni, Yehova anaona kuti akung’ung’udzira Iyeyo
-
Yoh 6:41-69—Ayuda ankang’ung’udza za Yesu; ophunzira ake ena anamusiya
-
Nthabwala zotukwana
Zolaula
Onani “Zolaula”
Kukangana
Kunyoza
Onaninso Miy 17:5; 22:10; 2Pe 3:3, 4
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
2Mb 36:15-21—Anthu a Mulungu opanduka analangidwa koopsa chifukwa chonyoza atumiki komanso aneneri a Mulungu
-
Yob 12:4; 17:2; 21:3; 34:7—Yobu yemwe anali munthu wolungama ananyozedwa pa nthawi yomwe ankakumana ndi mayesero ovuta
-
Kuba
Onani “Kuba”
Mikangano; chiwawa
Onaninso 1Ti 3:2, 3; Tit 1:7
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Eks 21:22-27—Chilamulo cha Mose chinkanena kuti munthu akamachita zachiwawa ndi kuvulaza kapena kupha mnzake, azipatsidwa chilango
-
Kuopseza
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Mac 4:15-21—Khoti la Sanihedirini linaopseza ophunzira a Yesu pofuna kuti asiye kugwira ntchito yolalikira
-
Maphwando aphokoso