Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zimene Zili M’magazini Ino

Zimene Zili M’magazini Ino

Zimene Zili M’magazini Ino

● Kodi ndi mfundo 7 ziti zimene zingathandize banja lanu kuti liziyenda bwino? Onani tsamba 3 mpaka 9.

● Kodi achinyamata angatani kuti aziwadziwa bwino makolo awo? Onani tsamba 10 mpaka 13.

● Kodi ndi bwino kuti mwamuna ndi mkazi amene sanakwatirane azikhalira limodzi? Onani tsamba 28 ndi 29

● Ngati mukulera nokha ana, kodi n’chiyani chimene chingakuthandizeni kuti muwalere bwino? Onani tsamba 26 ndi 27.

● Ngati banja latha, kodi ana angathandizidwe bwanji? Onani tsamba 18 mpaka 21.

Amenewa ndi ena mwa mafunso okhudza banja amene ayankhidwa mu “Galamukani!” yapaderayi.

Ngati mukufuna kudziwa zambiri, lembani zofunika m’mizere ili m’munsiyi, ndipo tumizani ku adiresi yomwe ili pomwepoyo kapena tumizani ku adiresi yoyenera patsamba 5 la magazini ino.

□ Ndikupempha kuti munditumizire bukuli.

□ Nditumizireni munthu kuti ayambe kuphunzira nane Baibulo kwaulere.