Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zinthu Zidzasinthadi Kodi Inuyo Mudzakhalako?

Zinthu Zidzasinthadi Kodi Inuyo Mudzakhalako?

Zinthu Zidzasinthadi Kodi Inuyo Mudzakhalako?

● Nkhani zoyambirira m’magazini ino zasonyeza kuti anthu ambiri padziko lonse amafuna zinthu zitasintha. Kodi inuyo mudzakhalako zinthu zikadzasintha padzikoli?

A Mboni za Yehova, omwe amafalitsa magazini ino amakhulupirira kuti Baibulo lingatithandize kudziwa zimene zidzachitike m’tsogolo. Baibulo ndi buku lokhalo limene limafotokoza mbiri ya anthu kuyambira pamene munthu analengedwa. Komanso mosiyana ndi zimene anthu ambiri amakhulupirira, Baibulo limafotokoza kuti m’tsogolomu zinthu zidzakhala bwino.

Buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lingakuthandizeni kudziwa zambiri zimene Baibulo limafotokoza pa nkhani imeneyi. Bukuli limafalitsidwa ndi Mboni za Yehova ndipo lamasuliridwa m’zinenero 244.

□ Ndikupempha kuti munditumizire bukuli. Lembani chinenero chimene mukufuna.

□ Nditumizireni munthu kuti ayambe kuphunzira nane Baibulo kwaulere.