NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) July 2024
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira September 9–October 6, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 27
Muzikhala Olimba Mtima Ngati Zadoki
Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 9-15, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 28
Kodi Mumatha Kuzindikira Choonadi?
Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 16-22, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 29
Tiyenera Kukhala Maso Kuti Tizipewa Mayesero
Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 23-29, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 30
Zimene Tikuphunzira kwa Mafumu a Chiisiraeli
Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 30–October 6, 2024.
Kodi Mungatani Kuti Muzolowere Mukasamukira Mumpingo Wina?
Akhristu ambiri zimawayendera bwino akasamukira mumpingo watsopano. Kodi n’chiyani chingakuthandizeni ngati mwasamukira mumpingo wina? Onani mfundo 4 zimene zingakuthandizeni kuti muzolowere msanga mpingo watsopanowo.
Mafunso Ochokera kwa Owerenga
Kodi “mkazi” wotchulidwa pa Yesaya 60:1 ndi ndani, nanga ‘anaimirira’ bwanji komanso anaonetsa bwanji “kuwala”?