Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Moyo wabwino kwambiri

Moyo wabwino kwambiri

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Dziko limaonetsa ngati

    Ndilibe anzanga.

    Timathandizansotu ena kupeza mabwenzi.

    N’kamadera nkhawa, sizingathandize.

    Ndimamvako bwino ndikathandiza ena.

    Ndizomwe ndawona.

    (KOLASI)

    Angandiuzeko ndani: Ndikhale moyo wotani?

    Moyo wabwino zedi

    Angatsutsenso ndani? Moyo weniweni.

    Moyo wabwino zedi.

  2. 2. Palitu zambili zochita, ndi manja angawa.

    Ndidzasonyezanso chikondi—⁠kwa abale anga.

    N’kamadera nkhawa, sizingathandize,

    Ndimamvako bwino ndikathandiza ena

    Ndizomwe ndaona.

    (KOLASI)

    Angandiuzeko ndani: Ndikhale moyo wotani?

    Moyo wabwino zedi

    Angatsutsenso ndani? Moyo weniweni.

    Moyo wabwino.

    (VESI LOKOMETSERA)

    Sindiopa zamawa.

    Nthawi zonse, ndi moyo wabwino—wabwino, wabwino.

    (KOLASI)

    Angandiletsenso ndani? Ine ndadzipelekadi.

    Moyo wabwino zedi

    Angatsutsenso ndani? Tadzaoneni;

    Moyo wabwino zedi.

    Moyo wabwino zedi.

    Moyo wabwino zedi.