Mfundo Zachidule—Armenia
- 3,103,000—Chiwerengero cha anthu
- 11,313—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 134—Mipingo
- Pa anthu 277 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
Boma la Armenia Lazindikira Kuti Anthu Okana Usilikali Ali Ndi Ufulu
Zimene Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Europe lakhala likugamula, zathandiza kwambiri dziko la Armenia pa nkhani yopereka ntchito zina kwa anthu okana usilikali ndipo panopa zinthu zikuyenda bwino.
NKHANI
Gulu Loyamba la Mboni za Yehova ku Armenia Lamaliza Kugwira Ntchito Zimene Linapatsidwa Litakana Kulowa Usilikali
Panopo a Mboni ku Armenia angathe kugwira ntchito zimene sizikusemphana ndi zomwe amakhulupirira ndipo ntchitozo zimathandiza anthu ambiri.
NKHANI
Dziko la Armenia Latulutsa M’ndende Anthu Amene Anamangidwa Chifukwa Chokana Kulowa Usilikali
Kodi chinachitika n’chiyani pa mlandu wokhudza kumangidwa kwa anthu a Mboni za Yehova mpaka kutulutsidwa kwawo m’ndende?