Mfundo Zachidule—Canada
- 38,704,000—Chiwerengero cha anthu
- 120,388—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 1,164—Mipingo
- Pa anthu 325 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
Khoti Lalikulu Kwambiri ku Canada Lagamula Kuti Makhoti Sayenera Kulowerera Dongosolo Lochotsa Munthu Mumpingo
Khoti Lalikulu Kwambiri ku Canada linanena kuti dongosolo lochotsa munthu mumpingo ‘‘si lankhanza koma cholinga chake n’kuthandiza munthuyo kuti abwererenso mumpingo.’’
NTCHITO YOLALIKIRA
Akulalikira Anthu Amitundu Yosiyanasiyana ku Canada
A Mboni za Yehova amalalikira m’zilankhulo zosiyanasiyana n’cholinga choti anthu aphunzire za Mlengi wathu m’chilankhulo chawo.