Mfundo Zachidule—Malawi
- 20,728,000—Chiwerengero cha anthu
- 109,108—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 1,882—Mipingo
- Pa anthu 211 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Ndinalola Kuti Yehova Azinditsogolera pa Moyo Wanga
Mbiri ya Moyo Wanga: Keith Eaton
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Kuonera Kapena Kumvetsera Msonkhano
Msonkhano wachigawo wa chaka cha 2020 unaikidwa pa intaneti, koma anthu ambiri ku Malawi ndi ku Mozambique sangakwanitse kugwiritsa ntchito intaneti. Ndiye kodi anatha bwanji kumvetsera msonkhanowu?
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Tchanelo cha JW Setilaiti Chimaoneka Kumene Kulibe Intaneti
Kodi abale a ku Africa amatani kuti aonere JW Broadcasting ngati alibe intaneti?
NKHANI
Kampeni Yolemba Makalata M’malo mwa Abale Athu ku Russia—Kuchokera ku Malawi
A Mboni za Yehova ku Malawi akufotokoza zimene zinawachititsa kuti apange nawo kampeni yolemba makalata ya posachedwapa pofuna kuthandiza abale awo ku Russia.
NKHANI
Ana Awiri a Mboni za Yehova Anawalola Kuyambiranso Sukulu Atawachotsa Chifukwa cha Zimene Amakhulupirira
Ana awiri a Mboni za Yehova anawachotsa sukulu chifukwa chokana kuimba nawo nyimbo ya fuko. Akuluakulu a pasukulupo anawalola kuti ayambirenso sukulu.
NTCHITO YOFALITSA MABUKU
Kuthandiza Anthu Amene Ali ndi Vuto Losaona, ku Africa
Anthu omwe ali ndi vuto losaona ku Malawi akuyamikira Yehova chifukwa cholandira mabuku ophunzirira Baibulo a zilembo zawo m’Chichewa.