Mfundo Zachidule—Nigeria
- 222,182,000—Chiwerengero cha anthu
- 400,375—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 6,071—Mipingo
- Pa anthu 589 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Tchanelo cha JW Setilaiti Chimaoneka Kumene Kulibe Intaneti
Kodi abale a ku Africa amatani kuti aonere JW Broadcasting ngati alibe intaneti?
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Makolo Anga Anandithandiza Kuti Ndizitumikira Yehova
Sangalalani ndi mbiri ya moyo wa Woodworth Mills, amene watumikira Yehova mokhulupirika kwa zaka pafupifupi 80.
NTCHITO ZOMANGAMANGA
A Mboni za Yehova ku Nigeria Amanga Nyumba za Ufumu Zokwana 3,000
A Mboni za Yehova ku Nigeria anachita msonkhanowu pokumbukira kuti m’dzikoli mwamangidwa Nyumba za Ufumu 3,000. Pa mwambowu panafotokozedwa mbiri yachidule yokhudza ntchito ya a Mboni za Yehova m’dzikoli kuyambira m’ma 1920.