Mfundo Zachidule—Papua New Guinea
- 9,466,000—Chiwerengero cha anthu
- 5,692—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 89—Mipingo
- Pa anthu 1,999 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
KALE LATHU
Boti la Lightbearer Linabweretsa Kuwala kwa Choonadi Kum’mwera Chakum’mawa kwa Asia
Ngakhale kuti ankatsutsidwa, amuna ochepa a m’boti la Lightbearer anafalitsa molimba mtima kuwala kwa choonadi cha m’Baibulo m’dera lalikulu kwambiri lokhala anthu ambiri.