NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA October 2024
Magazini ino ili na nkhani zophunzila mu mlungu wa December 9, 2024–January 5, 2025.
1924—Zaka 100 Zapitazo
M’caka ca 1924, Ophunzila Baibo anagwilitsila nchito njila zatsopano kuti apitilize kulalikila uthenga wabwino molimba mtima.
NKHANI YOPHUNZILA 40
Yehova “Amacilitsa Anthu Osweka Mtima”
Yophunzila mu mlungu wa December 9-15, 2024.
NKHANI YOPHUNZILA 41
Zimene Yesu Anacita M’masiku Ake 40 Othela Padziko Lapansi
Yophunzila mu mlungu wa December 16-22, 2024.
NKHANI YOPHUNZILA 42
Muzionetsa kuti Mumayamikila “Mphatso za Amuna”
Yophunzila mu mlungu wa December 23-29, 2024.
NKHANI YOPHUNZILA 43
Mmene Tingathetsele Zikaiko Zathu
Yophunzila mu mlungu wa December 30, 2024–January 5, 2025.
Kodi Mudziŵa?
Kodi nyimbo zinali zofunika motani kwa Aisiraeli akale?
Mafunso Ocokela Kwa Oŵelenga
Kodi khonde la kacisi wa Solomo linali lalitali motani?
Muzibwelelamo mu Mfundo Zikulu-zikulu
Kodi mumavutika kukumbukila zimene mwacoka kuŵelenga? N’ciyani cingakuthandizeni kuti muzikumbukila zimene mwaŵelenga?