NSANJA YA MLONDA January 2014 | Kodi Imfa Ndi Mapeto a Zonse?

Anthu ambili sakonda kukambitsilana za imfa. Kunena zoona, anthu safuna kufa. Kodi imfa ingagonjetsedwe?

NKHANI YA PACIKUTO

Mphamvu ya Imfa

Tonsefe tingakhudzidwe ndi imfa nthawi iliyonse. Ululu wake wacititsa anthu ambili kufunsa mafunso okhudza imfa.

NKHANI YA PACIKUTO

Zimene Anthu Acita Pofuna Kugonjetsa Imfa

M’mbili yonse, anthu afuna-funa njila zogonjetsela imfa. Kodi n’zotheka kugonjetsa imfa?

NKHANI YA PACIKUTO

Imfa Si Mapeto a Zonse

N’cifukwa ciani Yesu anayelekezela imfa ndi tulo? Kodi timaphunzila ciani pankhani za kuuka kwa akufa zolembedwa m’Baibo?

KUKAMBILANA NDI MUNTHU WINA

N’cifukwa Ciani Mulungu Amalola Kuti Anthufe Tizivutika?

Buku loyambilila la m’Baibo limafotokoza cifukwa cake Mulungu walola kuti anthu azivutika ngakhale kuti ali na mphamvu zothetsela mavuto.

Lambilani Yehova, Mfumu Yamuyaya

Kuphunzila mmene Yehova amacitila zinthu monga Tate ndiponso monga mfumu kudzatithandiza kumuyandikila kwambili.

Kodi Ulamulilo wa Yesu wa Zaka 100 Wakupindulitsani Bwanji?

Kodi tingapindule motani ndi ulamulilo wa Ufumu? Phunzilani mmene Mfumu Mesiya amayengela, kuphunzitsa, ndi kulinganiza atumiki ake a padziko lapansi.

Pangani Zosankha Mwanzelu Mukali Acinyamata

Acinyamata ambili odzipeleka akusangalala kuthandiza ena kumvetsetsa coonadi. Kodi mungacite ciani kuti mugwile nao nchito yosangalatsa mu utumiki wa Yehova?

Tumikilani Yehova Asanafike Masiku Oipa

Kodi Akristu okalamba ali ndi mipata yapadela iti yoonjezela utumiki wao?

“Ufumu Wanu Ubwele”—Kodi Udzabwela Liti?

N’cifukwa ciani timakhulupilila kuti posacedwapa Mfumu yodzozedwa ya Mulungu idzakwanilitsa cifunilo ca Mulungu padziko lapansi?

Kuyankha Mafunso a m’Baibo

Kodi mumadziŵa zotani zokhudza Mulungu? Kodi tingacite ciani kuti tim’dziŵe bwino?