Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.
Suriname
Garnizoenspad 239
DISTRICT WANICA
SURINAME
+597 328054
+597 328049
+597 328021
+597 328019
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.
Nthawi yoona malo: Mphindi 45
Zimene Timacita
Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova m’dzikoli. Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’zinenelo 5, kuphatikizapo cinenelo ca manja ca ku Suriname. Timapanganso ma CD a zofalitsa za zinenelo zambili.