Onani zimene zilipo

MARCH 15, 2024
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2024

Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2024

Mu ciunikilo cino, tione mmene Atate wathu Yehova amaonetsela kuti “akufuna kuti anthu onse alape.” (2 Pet. 3:9) Tionenso masinthidwe amene apangidwa pa nkhani ya mavalidwe athu pamene tili ku misonkhano ya mpingo kapena ikulu-ikulu.